{"product_id":"2940046637434","title":"Rhapsodie der Realität: MÄRZ 2015 German Edition","description":"\u003cp\u003eThe Rhapsodie der Realität TeeVo anapangidwa, kuti akatakase, kulimbikitsa, kupereka nyonga kwa inu. Popereka mayankho kuchokera m’Mawu a Mulungu-kumafunso amene amakuzunguzani, buku ili likuthandizani kupeza cholinga chenicheni cha moyo wanu wachipambano.\u003cbr\u003ePowerenga, buku la TeeVo looneka mochititsa kasoli, padzakhala kusinthana maganizo, chisangalalo, komanso nkhani zokutakasani inu kuti mukalimbikitsidwe m’moyo mwanu komanso m’maganizo anu. izi ndi monga *Zamphamvu zomwe anayankhula alembi *Mafunso * Masewera ogwiritsa ntchito ubongo * Mfundo za “Kodi mukudziwa?” *Maumboni wochititsa chidwi * Galo la Mawu – apa ndi pamene matanthauzo a mawu osiyanasiyana amaperekedwa.\u003cbr\u003eNdi buku lodzadza ndi nkhani zimene zingakuthandizeni inu kukhala wokondwa m’Mawu a Mulungu.\u003c\/p\u003e","brand":"LoveWorld Publishing","offers":[{"title":"Default Title","offer_id":47067856896240,"sku":"2940046637434","price":2.5,"currency_code":"USD","in_stock":true}],"thumbnail_url":"\/\/cdn.shopify.com\/s\/files\/1\/0737\/7593\/9824\/files\/2940046637434_p0.jpg?v=1763697226","url":"https:\/\/shop-qa.barnesandnoble.com\/products\/2940046637434","provider":"Barnes \u0026 Noble (DEV)","version":"1.0","type":"link"}