Skip to product information
1 of 1

LoveWorld Publishing

Rhapsodie der Realität: MÄRZ 2015 German Edition

Rhapsodie der Realität: MÄRZ 2015 German Edition

Regular price $2.50 USD
Regular price Sale price $2.50 USD
Sale Sold out
Shipping calculated at checkout.
Quantity

The Rhapsodie der Realität TeeVo anapangidwa, kuti akatakase, kulimbikitsa, kupereka nyonga kwa inu. Popereka mayankho kuchokera m’Mawu a Mulungu-kumafunso amene amakuzunguzani, buku ili likuthandizani kupeza cholinga chenicheni cha moyo wanu wachipambano.
Powerenga, buku la TeeVo looneka mochititsa kasoli, padzakhala kusinthana maganizo, chisangalalo, komanso nkhani zokutakasani inu kuti mukalimbikitsidwe m’moyo mwanu komanso m’maganizo anu. izi ndi monga *Zamphamvu zomwe anayankhula alembi *Mafunso * Masewera ogwiritsa ntchito ubongo * Mfundo za “Kodi mukudziwa?” *Maumboni wochititsa chidwi * Galo la Mawu – apa ndi pamene matanthauzo a mawu osiyanasiyana amaperekedwa.
Ndi buku lodzadza ndi nkhani zimene zingakuthandizeni inu kukhala wokondwa m’Mawu a Mulungu.

View full details